top of page
Maphunziro Acikristu.jpg

MAPHUNZIRO
ACIKRISTU

Maphunziro a anyamata ndi atsikana,

makolo ndi anthu okwatirana

Maphunziro a anyamata ndi atsikana
(a zaka 12-17)

1. Colinga ca miyoyo yathu

2. Kuthetsa mabvuto

3. Ubwenzi

4. Kukakamizidwa ndi abwenzi

5. Kusamalira thupi langa ndi cilengedwe

6. Cikhalidwe 

7. Tsogolo langa

​

Tengani maphunziro APA. 

Maphunziro a anyamata ndi atsikana

(a zaka 18-35)

1. Colinga ca miyoyo yathu ndi kupanga maganizo

2. Kukakamizidwa ndi abwenzi

3. Ubwenzi

4. Matupi athu ndiwo mphatso zocokera kwa Mulungu

5. Cikondi ndi ukwati

6. Kupewa mayesero

​

Tengani maphunziro APA.

Pemphero la Ambuye

1. Atate wathu wa Kumwamba

2. Dzina lanu liyeretsedwe

3. Ufumu wanu udze

4. Kufuna kwanu kucitidwe

5. Mutipatse ife lero cakudya cathu calero

6. Mutikhululukire mangawa athu monga ifenso takhululukira amangawa anthu

7. Musatitengere ife kokatiyesa koma mutipulumutse kwa woipayo

​

Tengani maphunziro APA.

Imani nji! Cikhulupiriro ca Atumwi

1. Ndikhulupirira Mulungu
2. Atate wamphamvu wa mphamvu zonse, wakulenga za kumwamba ndi za pansi.
3. Ndikhulupirira Yesu Kristu, Mwana wake wobadwa yekha, Ambuye wathu
4. Amene anapatsidwa ndi Mzimu Woyera, nabadwa mwa Mariya namwaliyo, nasautsidwa kwa Pontio Pilato
5. Namwalira, naikidwa m’manda
6. Natsikira kwa akufa. Tsiku lacitatu anaukanso kwa akufa
7. Nakwera Kumwamba, nakhala padzanja lamanja la Mulungu Atate wa mphamvu zonse, kucokera komweko adzadzakudzaweruza anthu amoyo ndi akufa.
8. Ndikhulupirira Mzimu Woyera. Ndikhulupirira Mpingo wopatulika wa Kristu wa kwa anthu onse
9. Ciyanjano ca oyera mtima, kukhululukidwa kwa macimo
10. Kuukanso kwa thupi, ndi moyo wosatha. Amen.

​

Tengani maphunziro APA.

Mabanja acikristu

(maphunziro a anthu opezeka m’ukwati ndi a makolo)

1. Maziko a ukwati wacikristu

2. Ukwati wacikristu

3. Azimuna acikristu

4. Azimai acikristu

5. Makolo acikristu monga zitsanzo

6. Makolo acikristu monga aziphunzitsi

7. Mabanja acikristu 

​

Tengani maphunziro APA.

Umoyo wacikristu

1. Baibulo

2. Thanzi ndi matenda

3. Cuma ndi umphawi

4. Mdima ndi Kuunika

5. Pemphero

6. Coonadi ndi cinyengo

​

Tengani maphunziro APA.

  • YouTube

Kulembanso zinthu ndi colinga copangirapo ndalama sikuloledwa.

©2026 Stephanos Zambia Trust

Mfundo yosunga zisinsi

bottom of page