top of page

Mau ofanana ndi mau obvuta opezeka m'Baibulo la m'Chichewa

Bukuli ndi la aliyense wokonda kuphunzira za m'Baibulo.

M'Bukuli mupeza mau ofanana ndi mau osadziwika a m'Baibulo la m'Chichewa.

Tengani buku APA.

Mau a masiku onse

Buku iri lidzakutsogolerani m’Baibulo ndi zowerenga za tsiku lirilonse ndi mau ofotokozera ndime za m’Baibulo.

Tengani buku APA.

Mupangiridwa kulemba mbali zonse ziwiri.

Katekisma wa Heidelberg

Katekisma wa Heidelberg itiphunzitsa mfundo zikulu-zikulu za m'Baibulo.

Tengani Katekisma wa Heidelberg (Chichewa-Cingerezi) APA.

Zitanthauzo za mau ogwiritsidwa nchito m'Cikristu

Tengani mau APA.

  • YouTube

Kulembanso zinthu ndi colinga copangirapo ndalama sikuloledwa.

©2026 Stephanos Zambia Trust

Mfundo yosunga zisinsi

bottom of page